Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 15:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Kuwonjezera apo, pamene Abisalomu anali kupereka nsembe, anaitanitsa Ahitofeli+ Mgilo,+ phungu wa Davide,+ kuchoka kumzinda wakwawo wa Gilo.+ Chiwembu+ chimenecho chinapitiriza kukula ndipo chiwerengero cha anthu amene anali kutsatira Abisalomu chinapitiriza kuwonjezeka.+

  • 2 Samueli 16:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ndiyeno masiku amenewo munthu akalandira malangizo kwa Ahitofeli, zinali ngati kuti munthu wafunsira malangizo kwa Mulungu woona. Umu ndi mmene malangizo+ onse a Ahitofeli+ analili, kwa Davide ndi Abisalomu yemwe.

  • Yeremiya 9:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Aliyense wa inu asamale ndi mnzake,+ ndipo musakhulupirire m’bale aliyense.+ Pakuti munthu aliyense amalanda malo a m’bale wake,+ ndipo munthu aliyense amakhala akuyendayenda kunenera mnzake miseche.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena