Deuteronomo 32:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kumbukirani masiku akale,+Ganizirani zaka za mibadwomibadwo ya m’mbuyomu.Funsa bambo ako ndipo akuuza,+Amuna achikulire pakati panu, ndipo akufotokozera.+ Salimo 143:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndakumbukira masiku akale.+Ndasinkhasinkha zochita zanu zonse,+Ndipo ndakhala ndikuganizira ntchito ya manja anu ndi mtima wonse.+ Yesaya 51:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Dzuka! Dzuka! Vala mphamvu,+ iwe dzanja la Yehova!+ Dzuka ngati masiku akale, ngati m’mibadwo yakalekale.+ Kodi si iwe amene unaphwanyaphwanya Rahabi,+ amene unabaya* chilombo cha m’nyanja?+ Yesaya 63:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamene iwo anali kuvutika m’masautso awo onse, iyenso anali kuvutika.+ Mthenga amene iye anawatumizira, anawapulumutsa.+ Chifukwa cha chikondi chake ndi chisoni chake, iye anawawombola.+ Anawakweza m’mwamba ndi kuwanyamula masiku onse akale.+
7 Kumbukirani masiku akale,+Ganizirani zaka za mibadwomibadwo ya m’mbuyomu.Funsa bambo ako ndipo akuuza,+Amuna achikulire pakati panu, ndipo akufotokozera.+
5 Ndakumbukira masiku akale.+Ndasinkhasinkha zochita zanu zonse,+Ndipo ndakhala ndikuganizira ntchito ya manja anu ndi mtima wonse.+
9 Dzuka! Dzuka! Vala mphamvu,+ iwe dzanja la Yehova!+ Dzuka ngati masiku akale, ngati m’mibadwo yakalekale.+ Kodi si iwe amene unaphwanyaphwanya Rahabi,+ amene unabaya* chilombo cha m’nyanja?+
9 Pamene iwo anali kuvutika m’masautso awo onse, iyenso anali kuvutika.+ Mthenga amene iye anawatumizira, anawapulumutsa.+ Chifukwa cha chikondi chake ndi chisoni chake, iye anawawombola.+ Anawakweza m’mwamba ndi kuwanyamula masiku onse akale.+