Yobu 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye waika abale anga enieni kutali ndi ine,+Ndipo ngakhale anthu ondidziwa andisiya. Salimo 31:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndakhala chitonzo+ pamaso pa onse odana nane,+Ndipo kwa anthu oyandikana nawo ndakhala chitonzo chachikulu,+Kwa anthu ondidziwa ndakhala woopsa.+Akandiona ndili panja amandithawa.+ Salimo 38:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu amene anali kundikonda ndiponso anzanga aima patali chifukwa cha kuvutika kwanga,+Ndipo mabwenzi anga apamtima anditalikira.+ Salimo 88:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anzanga mwawaika kutali ndi ine.+Mwandisandutsa chinthu chonyansa kwa iwo.+Ndatsekerezedwa ndipo sindingathenso kuchoka.+
11 Ndakhala chitonzo+ pamaso pa onse odana nane,+Ndipo kwa anthu oyandikana nawo ndakhala chitonzo chachikulu,+Kwa anthu ondidziwa ndakhala woopsa.+Akandiona ndili panja amandithawa.+
11 Anthu amene anali kundikonda ndiponso anzanga aima patali chifukwa cha kuvutika kwanga,+Ndipo mabwenzi anga apamtima anditalikira.+
8 Anzanga mwawaika kutali ndi ine.+Mwandisandutsa chinthu chonyansa kwa iwo.+Ndatsekerezedwa ndipo sindingathenso kuchoka.+