Deuteronomo 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu wa milungu+ ndi Mbuye wa ambuye.+ Iye ndi Mulungu wamkulu, wamphamvu ndi woopsa,+ amene sakondera+ munthu aliyense ndipo salandira chiphuphu.+ Nehemiya 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamenepo ndinati: “Inu Yehova Mulungu wakumwamba, ndinu Mulungu wamkulu ndi wochititsa mantha.+ Anthu amene amakukondani+ ndi kusunga malamulo anu+ mumawasungira pangano+ ndi kuwasonyeza kukoma mtima kosatha. Salimo 76:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu ndinu wochititsa mantha,+Ndani angaime pamaso panu inu mutakwiya kwambiri?+ Salimo 95:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti Yehova ndi Mulungu wamkulu,+Ndiponso ndi Mfumu yaikulu kuposa milungu ina yonse.+
17 Pakuti Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu wa milungu+ ndi Mbuye wa ambuye.+ Iye ndi Mulungu wamkulu, wamphamvu ndi woopsa,+ amene sakondera+ munthu aliyense ndipo salandira chiphuphu.+
5 Pamenepo ndinati: “Inu Yehova Mulungu wakumwamba, ndinu Mulungu wamkulu ndi wochititsa mantha.+ Anthu amene amakukondani+ ndi kusunga malamulo anu+ mumawasungira pangano+ ndi kuwasonyeza kukoma mtima kosatha.