Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 5:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Pamenepo Elisa anati: “Kodi mtima wanga sunali nawe limodzi pamene munthuyo anali kutembenuka ndi kutsika pagaleta lake kuti akumane nawe? Kodi ino ndi nthawi yolandira siliva, zovala, minda ya maolivi, minda ya mpesa, nkhosa, ng’ombe, antchito aamuna, kapena antchito aakazi?+

  • Machitidwe 1:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “Amuna inu, abale, kudzera pakamwa pa Davide, mzimu woyera+ unaneneratu lemba lokhudza Yudasi,+ amene anatsogolera anthu okagwira Yesu.+ Kunali kofunikira kuti lembalo likwaniritsidwe+

  • Machitidwe 5:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Koma Petulo anati: “Hananiya, n’chifukwa chiyani Satana+ wakulimbitsa mtima choncho kuti uyese kunamiza+ mzimu woyera+ ndi kubisa zina mwa ndalama za mtengo wa mundawo?

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena