Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 24:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Choncho Mose analemba mawu onse a Yehova.+ Ndiyeno anadzuka m’mawa kwambiri n’kumanga guwa lansembe ndi zipilala 12 zoimira mafuko 12 a Isiraeli, m’tsinde mwa phiri.+

  • Numeri 12:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndimalankhula naye pamasom’pamaso,+ kumuuza zinthu momveka bwino osati mophiphiritsa,+ ndipo amaona maonekedwe a Yehova.+ Tsopano n’chifukwa chiyani inu simunaope kum’nena Mose mtumiki wanga?”+

  • Deuteronomo 34:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma mu Isiraeli simunakhalebe mneneri aliyense wofanana ndi Mose,+ amene Yehova anali kumudziwa pamasom’pamaso,+

  • Nehemiya 9:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Munawaphunzitsa za sabata lanu lopatulika.+ Munawapatsa malangizo, mfundo ndi chilamulo kudzera mwa Mose mtumiki wanu.+

  • Machitidwe 7:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Mose ameneyo, amene iwo anamukana ndi kunena kuti, ‘Iweyo anakuika ndani kuti ukhale wolamulira ndi woweruza wathu?’+ munthu ameneyo ndi amene Mulungu anamutumiza+ monga wolamulira ndi mpulumutsi kudzera mwa mngelo amene anaonekera kwa iye pachitsamba chaminga chija.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena