Salimo 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chilamulo+ cha Yehova ndi changwiro,+ chimabwezeretsa moyo.+Zikumbutso+ za Yehova ndi zodalirika,+ zimapatsa nzeru munthu wosadziwa zinthu.+ Salimo 119:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndimakondwera kuyenda m’njira ya zikumbutso zanu,+Ngati mmene anthu amachitira akapeza chuma chilichonse chamtengo wapatali.+ Salimo 119:168 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 168 Ndasunga malamulo anu ndi zikumbutso zanu,+Pakuti njira zanga zonse zili pamaso panu.+
7 Chilamulo+ cha Yehova ndi changwiro,+ chimabwezeretsa moyo.+Zikumbutso+ za Yehova ndi zodalirika,+ zimapatsa nzeru munthu wosadziwa zinthu.+
14 Ndimakondwera kuyenda m’njira ya zikumbutso zanu,+Ngati mmene anthu amachitira akapeza chuma chilichonse chamtengo wapatali.+