Salimo 31:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Inu Yehova, musalole kuti ndichite manyazi, pakuti ndaitana pa dzina lanu.+Anthu oipa achite manyazi.+Akhale chete m’Manda.+ Salimo 88:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Diso langa lafooka chifukwa cha kusautsika kwanga.+Ndaitana inu Yehova tsiku lonse.+Ndapemphera kwa inu nditakweza manja anga.+
17 Inu Yehova, musalole kuti ndichite manyazi, pakuti ndaitana pa dzina lanu.+Anthu oipa achite manyazi.+Akhale chete m’Manda.+
9 Diso langa lafooka chifukwa cha kusautsika kwanga.+Ndaitana inu Yehova tsiku lonse.+Ndapemphera kwa inu nditakweza manja anga.+