Numeri 6:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Yehova akuyang’aneni mokondwera+ ndipo akupatseni mtendere.”’+ Salimo 80:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu Mulungu wa makamu, tibwezeretseni mwakale.+Walitsani nkhope yanu kuti tipulumutsidwe.+ Salimo 89:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Odala ndi anthu amene amafuula mosangalala.+Iwo amayendabe m’kuwala kwa nkhope yanu, inu Yehova.+ Salimo 119:135 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 135 Ndikomereni mtima ine mtumiki wanu,+Ndipo ndiphunzitseni malamulo anu.+ Miyambo 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Nkhope ya mfumu ikawala, zimatanthauza moyo.+ Ndipo mafuno ake abwino ali ngati mtambo wa mvula yomalizira.+ 1 Petulo 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti maso+ a Yehova* ali pa olungama, ndipo makutu ake amamva pembedzero lawo,+ koma nkhope ya Yehova imakwiyira anthu ochita zoipa.”+
15 Nkhope ya mfumu ikawala, zimatanthauza moyo.+ Ndipo mafuno ake abwino ali ngati mtambo wa mvula yomalizira.+
12 Pakuti maso+ a Yehova* ali pa olungama, ndipo makutu ake amamva pembedzero lawo,+ koma nkhope ya Yehova imakwiyira anthu ochita zoipa.”+