Yeremiya 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Onse pamodzi ndi opanda nzeru ndiponso opusa.+ Mtengo umangowalimbikitsa kuchita zachabechabe.+ Yona 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu okhulupirira mafano, amaleka kusonyeza kukoma mtima kwawo kosatha.+ 1 Akorinto 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno pa nkhani ya kudya+ zakudya zoperekedwa kwa mafano, timadziwa kuti fano ndi lopanda pake+ m’dziko, ndiponso kuti kulibe Mulungu wina koma mmodzi yekha.+
4 Ndiyeno pa nkhani ya kudya+ zakudya zoperekedwa kwa mafano, timadziwa kuti fano ndi lopanda pake+ m’dziko, ndiponso kuti kulibe Mulungu wina koma mmodzi yekha.+