Miyambo 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ukamvetsera nzeru ndi khutu lako,+ ukaika mtima wako pa kuzindikira,+ Miyambo 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mwana wanga, zimenezi zisachoke pamaso pako.+ Usunge nzeru zopindulitsa ndiponso kuganiza bwino,+ Miyambo 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munthu wopanda nzeru mumtima mwake amanyoza mnzake,+ koma munthu wozindikira bwino ndi amene amakhala chete.+ Danieli 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 amene analibe chilema chilichonse,+ ooneka bwino, ozindikira zinthu, anzeru,+ odziwa zinthu, omvetsa zinthu mwamsanga,+ amenenso akanatha kutumikira m’nyumba ya mfumu.+ Anawabweretsa kuti awaphunzitse kulemba* ndiponso chinenero cha Akasidi. Mateyu 24:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Choncho, mukadzaona chinthu chonyansa+ chowononga chimene chinanenedwa kudzera mwa mneneri Danieli chitaimirira m’malo oyera,+ (wowerenga adzazindikire,)
12 Munthu wopanda nzeru mumtima mwake amanyoza mnzake,+ koma munthu wozindikira bwino ndi amene amakhala chete.+
4 amene analibe chilema chilichonse,+ ooneka bwino, ozindikira zinthu, anzeru,+ odziwa zinthu, omvetsa zinthu mwamsanga,+ amenenso akanatha kutumikira m’nyumba ya mfumu.+ Anawabweretsa kuti awaphunzitse kulemba* ndiponso chinenero cha Akasidi.
15 “Choncho, mukadzaona chinthu chonyansa+ chowononga chimene chinanenedwa kudzera mwa mneneri Danieli chitaimirira m’malo oyera,+ (wowerenga adzazindikire,)