Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mlaliki 7:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Nzeru zimapangitsa munthu kukhala wamphamvu kuposa atsogoleri 10 amphamvu amene ali mumzinda.+

  • Danieli 1:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Pa nkhani iliyonse imene mfumu inali kufunsira nzeru kwa iwo kuti imvetse bwino,+ inaona kuti iwo anali anzeru kuwirikiza maulendo 10 kuposa ansembe onse ochita zamatsenga+ ndi anthu onse olankhula ndi mizimu+ amene anali mu ufumu wake.

  • Danieli 2:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Iye anati: “Dzina la Mulungu likhale lotamandika+ kuyambira kalekale mpaka kalekale, pakuti nzeru ndi mphamvu ndi zake.+

  • Danieli 5:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Mu ufumu wanu muli munthu amene ali ndi mzimu wa milungu yoyera.+ M’masiku a bambo anu, anthu anazindikira kuti munthuyu ndi wodziwa zinthu kwambiri, wozindikira ndiponso ali ndi nzeru zofanana ndi nzeru za milungu. Chotero bambo anu, Mfumu Nebukadinezara, anamuika kukhala mkulu+ wa ansembe ochita zamatsenga, anthu okhulupirira mizimu, Akasidi ndi anthu okhulupirira nyenyezi. Ndithudi mfumu, bambo anu anamupatsa udindo umenewu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena