Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 19:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Choncho mtumiki wangayo anandinenera+ ine mtumiki wanu miseche kwa inu mbuyanga mfumu. Koma inu mbuyanga mfumu muli ngati mngelo+ wa Mulungu woona, motero chitani zimene zili zabwino kwa inu.

  • Salimo 123:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Moyo wathu wasautsika kwambiri chifukwa cha kunyoza kwa anthu amene akukhala mosatekeseka,+

      Ndiponso chifukwa cha kunyoza kwa anthu odzikuza.+

  • Miyambo 18:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Mawu a munthu wonenera ena zoipa ali ngati zinthu zofunika kuzimeza msangamsanga,+ zimene zimatsikira mkatikati mwa mimba.+

  • 2 Akorinto 12:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ndikuopa kuti mwinamwake ndikadzafika,+ sindidzakupezani mmene ndikanafunira. Kwa inunso sindidzakhala mmene mukanafunira. M’malomwake, ndidzapeza ndewu, nsanje,+ kukwiyitsana, mikangano, miseche, manong’onong’o, kudzitukumula, ndi zisokonezo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena