Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 6:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pamenepo, Yehova anaona kuti kuipa kwa anthu kwachuluka padziko lapansi, ndipo malingaliro+ onse a m’mitima ya anthu anali oipa okhaokha nthawi zonse.+

  • Salimo 36:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Ali pabedi lake amakonza chiwembu kuti apweteke anzake.+

      Amaima panjira yoipa.+

      Sapewa kuchita zinthu zoipa.+

  • 1 Akorinto 10:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Tsopano zinthu zimenezi zinakhala zitsanzo kwa ife, kuti ifenso tisakhale anthu olakalaka zinthu zoipa+ ngati mmene iwo anachitira.

  • Agalatiya 6:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Musanyengedwe,+ Mulungu sapusitsika.+ Chilichonse chimene munthu wafesa, adzakololanso chomwecho.+

  • Yakobo 4:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Kapena mukuyesa kuti lemba limanena pachabe kuti: “Mzimu umene uli mwa ife uli ndi chizolowezi cholakalaka zinthu zosiyanasiyana”?+

  • 1 Yohane 2:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pakuti chilichonse cha m’dziko,+ monga chilakolako cha thupi,+ chilakolako cha maso+ ndi kudzionetsera ndi zimene munthu ali nazo pa moyo wake,+ sizichokera kwa Atate, koma kudziko.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena