-
1 Mafumu 16:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 M’chaka cha 26 cha Asa mfumu ya Yuda, Ela mwana wa Basa anakhala mfumu ya Isiraeli ku Tiriza kwa zaka ziwiri.
-
-
1 Mafumu 16:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Pomalizira pake, anthu amene anali kutsatira Omuri anagonjetsa otsatira Tibini mwana wa Ginati. Choncho Tibini anafa, ndipo Omuri anayamba kulamulira.
-