Salimo 37:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Yembekezera Yehova, ndi kusunga njira zake,+Ndipo adzakukweza kuti ulandire dziko lapansi.+Pamene oipa akuphedwa, iwe udzaona.+ Salimo 58:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Wolungama adzasangalala chifukwa chakuti waona oipa akupatsidwa chilango.+Adzasambitsa mapazi ake m’magazi a anthu oipa.+ Salimo 91:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Udzayang’ana ndi maso ako,+Ndipo udzaona anthu oipa akulandira chilango.+ Chivumbulutso 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Kondwerani kumwambako+ chifukwa cha zimene zamuchitikira. Inunso oyera,+ inu atumwi,+ ndi inu aneneri, kondwerani chifukwa Mulungu wamuweruza ndi kumupatsa chilango chifukwa cha zomwe anakuchitirani.”+
34 Yembekezera Yehova, ndi kusunga njira zake,+Ndipo adzakukweza kuti ulandire dziko lapansi.+Pamene oipa akuphedwa, iwe udzaona.+
10 Wolungama adzasangalala chifukwa chakuti waona oipa akupatsidwa chilango.+Adzasambitsa mapazi ake m’magazi a anthu oipa.+
20 “Kondwerani kumwambako+ chifukwa cha zimene zamuchitikira. Inunso oyera,+ inu atumwi,+ ndi inu aneneri, kondwerani chifukwa Mulungu wamuweruza ndi kumupatsa chilango chifukwa cha zomwe anakuchitirani.”+