Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 33:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndiyeno Yehova analankhulanso ndi Mose kuti: “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Inu ndinu anthu ouma khosi.+ Ndingathe kulowa pakati panu ndi kukufafanizani m’kamphindi.+ Chotero, vulani zodzikongoletsera, pakuti ndikufuna kuona choti ndikuchiteni.’”+

  • 2 Mbiri 29:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pakuti makolo athu achita zosakhulupirika+ ndipo achita zoipa pamaso pa Yehova Mulungu wathu.+ Iwo anamusiya+ n’kufulatira chihema chopatulika cha Yehova+ n’kulozetsako nkhongo.

  • Yeremiya 5:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Iwo akana Yehova, ndipo akunena kuti, ‘Iye kulibe.+ Ndipo ife tsoka silidzatigwera. Sitidzaona lupanga lililonse kapena njala yaikulu.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena