Yesaya 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chifukwa cha mkwiyo wa Yehova wa makamu, dzikolo layaka moto ndipo anthu adzakhala ngati chakudya cha motowo.+ Palibe amene adzamvere chisoni aliyense, ngakhale m’bale wake.+ Yeremiya 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndidzachititsa adani anu kutenga chumacho ndi kupita nacho kudziko limene simukulidziwa,+ pakuti mkwiyo wanga wayatsa moto.+ Ndithu, moto wakuyakirani anthu inu.” Yeremiya 17:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mwa kufuna kwanu munataya cholowa chimene ndinakupatsani.+ Inenso ndidzakuchititsani kutumikira adani anu m’dziko limene simunalidziwe.+ Anthu inu, ndakuyatsani ndi mkwiyo wanga+ ndipo moto wake udzayakabe mpaka kalekale.” Zefaniya 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Khalani chete pamaso pa Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa,+ pakuti tsiku la Yehova lili pafupi,+ ndipo Yehova wakonza nsembe+ moti wakonzekeretsa*+ anthu amene wawaitana.
19 Chifukwa cha mkwiyo wa Yehova wa makamu, dzikolo layaka moto ndipo anthu adzakhala ngati chakudya cha motowo.+ Palibe amene adzamvere chisoni aliyense, ngakhale m’bale wake.+
14 Ndidzachititsa adani anu kutenga chumacho ndi kupita nacho kudziko limene simukulidziwa,+ pakuti mkwiyo wanga wayatsa moto.+ Ndithu, moto wakuyakirani anthu inu.”
4 Mwa kufuna kwanu munataya cholowa chimene ndinakupatsani.+ Inenso ndidzakuchititsani kutumikira adani anu m’dziko limene simunalidziwe.+ Anthu inu, ndakuyatsani ndi mkwiyo wanga+ ndipo moto wake udzayakabe mpaka kalekale.”
7 Khalani chete pamaso pa Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa,+ pakuti tsiku la Yehova lili pafupi,+ ndipo Yehova wakonza nsembe+ moti wakonzekeretsa*+ anthu amene wawaitana.