Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 24:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Nebukadinezara mfumu ya Babulo, anabwera kudzachita nkhondo ndi mzindawo atumiki ake atauzungulira.+

  • 2 Mafumu 25:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 M’chaka cha 9+ cha ufumu wa Zedekiya, m’mwezi wa 10,+ pa tsiku la 10 la mweziwo, Nebukadinezara+ mfumu ya Babulo anabwera+ ku Yerusalemu pamodzi ndi gulu lake lonse lankhondo. Anabwera kudzachita nkhondo ndi mzindawo ndipo anamanga misasa ndi khoma kuzungulira mzinda wonsewo.+

  • Yeremiya 39:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 M’chaka cha 9 cha ulamuliro wa Zedekiya mfumu ya Yuda, m’mwezi wa 10,+ Nebukadirezara mfumu ya Babulo pamodzi ndi gulu lake lonse lankhondo anafika ku Yerusalemu ndi kuzungulira mzindawo.+

  • Ezekieli 4:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Uchite nkhondo ndi mzindawo+ ndipo umange mpanda womenyerapo nkhondo kuzungulira mzinda wonsewo.+ Umangenso chiunda chomenyerapo nkhondo*+ ndi misasa yokhalamo asilikali ankhondo. Uikenso zida zankhondo zowonongera mzindawo kuzungulira mzinda wonsewo.+

  • Ezekieli 21:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 M’dzanja lake lamanja, maulawo asonyeza kuti iye apite ku Yerusalemu, kuti akaike zida zogumulira mzindawo,+ akalamule asilikali ake kuti aphe anthu, akalize chizindikiro chochenjeza,+ akaike zida zogumulira zipata za mzindawo, ndiponso kuti akamange chiunda chomenyerapo nkhondo, ndi mpanda womenyerapo nkhondo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena