Yesaya 49:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Fuulani mokondwa kumwamba inu,+ ndipo sangalala iwe dziko lapansi.+ Mapiri asangalale ndipo afuule ndi chisangalalo.+ Pakuti Yehova watonthoza anthu ake+ ndipo amamvera chisoni anthu ake osautsidwa.+ Yeremiya 27:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘“‘Mtundu wa anthu umene udzaika khosi lake m’goli la mfumu ya Babulo ndi kuitumikira, ndidzauchititsa kukhala mwamtendere m’dziko lawo, ndipo adzalima minda ndi kukhalabe m’dzikomo,’ watero Yehova.”’”+
13 Fuulani mokondwa kumwamba inu,+ ndipo sangalala iwe dziko lapansi.+ Mapiri asangalale ndipo afuule ndi chisangalalo.+ Pakuti Yehova watonthoza anthu ake+ ndipo amamvera chisoni anthu ake osautsidwa.+
11 “‘“‘Mtundu wa anthu umene udzaika khosi lake m’goli la mfumu ya Babulo ndi kuitumikira, ndidzauchititsa kukhala mwamtendere m’dziko lawo, ndipo adzalima minda ndi kukhalabe m’dzikomo,’ watero Yehova.”’”+