Yeremiya 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Samala kuti phazi lako lisakhale lopanda nsapato, ndi kuti usachite ludzu.+ Koma iwe unati, ‘Zimenezo ayi!+ Ine ndakondana ndi alendo+ ndipo ndidzawatsatira.’+ Aroma 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma chifukwa chakuti ndiwe wosafuna kusintha khalidwe+ ndiponso wa mtima wosalapa,+ ukudzisungira mkwiyo wa Mulungu.+ Mulungu adzasonyeza mkwiyo+ umenewu pa tsiku loulula+ chiweruzo chake cholungama.+ Aheberi 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 M’malomwake, pitirizani kudandaulirana+ tsiku ndi tsiku, nthawi iliyonse imene mukuti “Lero,”+ kuopera kuti chinyengo+ champhamvu cha uchimo chingaumitse mtima wa wina wa inu.
25 Samala kuti phazi lako lisakhale lopanda nsapato, ndi kuti usachite ludzu.+ Koma iwe unati, ‘Zimenezo ayi!+ Ine ndakondana ndi alendo+ ndipo ndidzawatsatira.’+
5 Koma chifukwa chakuti ndiwe wosafuna kusintha khalidwe+ ndiponso wa mtima wosalapa,+ ukudzisungira mkwiyo wa Mulungu.+ Mulungu adzasonyeza mkwiyo+ umenewu pa tsiku loulula+ chiweruzo chake cholungama.+
13 M’malomwake, pitirizani kudandaulirana+ tsiku ndi tsiku, nthawi iliyonse imene mukuti “Lero,”+ kuopera kuti chinyengo+ champhamvu cha uchimo chingaumitse mtima wa wina wa inu.