Salimo 52:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Lilime lako limakonza chiwembu, ndipo ndi lakuthwa ngati lezala,+Limachita zachinyengo.+ Miyambo 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Imfa ndiponso moyo zili mu mphamvu ya lilime,+ ndipo wolikonda adzadya zipatso zake.+