Yesaya 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Vinyo watsopano akulira, ndipo mtengo wa mpesa wafota.+ Anthu onse amene anali kusangalala mumtima mwawo akuusa moyo.+ Ezekieli 26:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “‘Ndidzathetsa phokoso la kuimba kwako+ ndipo phokoso la azeze ako silidzamvekanso.+
7 Vinyo watsopano akulira, ndipo mtengo wa mpesa wafota.+ Anthu onse amene anali kusangalala mumtima mwawo akuusa moyo.+