Yesaya 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Dzikolo laipitsidwa ndi anthu okhalamo,+ chifukwa alambalala malamulo,+ asintha malamulowo+ ndipo aphwanya pangano limene linayenera kukhalapo mpaka kalekale.+ Yeremiya 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “M’kupita kwa nthawi, ndinakulowetsani m’dziko la minda ya zipatso kuti mudye zipatso zake ndi zinthu zabwino za m’dzikolo,+ koma munalowa m’dziko langa ndi kuliipitsa. Cholowa changa munachisandutsa chinthu chonyansa.+
5 Dzikolo laipitsidwa ndi anthu okhalamo,+ chifukwa alambalala malamulo,+ asintha malamulowo+ ndipo aphwanya pangano limene linayenera kukhalapo mpaka kalekale.+
7 “M’kupita kwa nthawi, ndinakulowetsani m’dziko la minda ya zipatso kuti mudye zipatso zake ndi zinthu zabwino za m’dzikolo,+ koma munalowa m’dziko langa ndi kuliipitsa. Cholowa changa munachisandutsa chinthu chonyansa.+