-
Esitere 4:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 “Pitani mukasonkhanitse Ayuda onse amene angapezeke ku Susani+ ndipo musale kudya+ m’malo mwa ine. Musadye kapena kumwa kwa masiku atatu,+ usana ndi usiku. Inenso pamodzi ndi atsikana anga onditumikira+ tisala kudya. Pamenepo, ngakhale kuti ndi zosemphana ndi lamulo, ndidzapita kwa mfumu, ndipo ngati n’kufa,+ ndife.”
-