Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 7:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Anaumba zipilala ziwiri zamkuwa.+ Kutalika kwa chipilala chilichonse kunali mikono 18, ndipo pankafunika chingwe chotalika mikono 12 kuti ayeze kuzungulira chipilala chilichonse.+

  • 2 Mafumu 25:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Koma panalibe njira yodziwira kulemera kwa mkuwa wa zipilala ziwiri zija, chosungiramo madzi chimodzi chija, ndi zotengera zokhala ndi mawilo zimene Solomo anapangira nyumba ya Yehova. Panalibe njira yodziwira kulemera kwa mkuwa wa ziwiya zonsezi.+

  • 2 Mbiri 4:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Anapanga zipilala ziwiri,+ mitu ya zipilala yozungulira+ imene anaiika pamwamba pa zipilala ziwirizo, ndiponso maukonde awiri+ okutira mitu iwiri yozungulira imene inali pamwamba pa zipilalazo.

  • Yeremiya 27:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 “Yehova wa makamu wanena mawu okhudza zipilala,+ thanki ya madzi,*+ zotengera zamawilo+ ndi ziwiya zotsala mumzinda uwu,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena