Salimo 115:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Manja ali nawo, koma sakhudza kanthu.+Mapazi ali nawo koma sayenda.+Satulutsa mawu ndi mmero wawo.+ Yesaya 46:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Beli+ wawerama+ ndipo Nebo wagwada. Mafano awo+ akhala katundu wa nyama zakutchire ndi wa nyama zoweta. Mafanowo angokhala katundu wolemera kwa nyama zotopa. Yesaya 46:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo amamunyamula pamapewa awo.+ Amamutenga n’kukamuika pamalo ake ndi kumuimika bwinobwino. Mulunguyo sayenda kuchoka pamalo akewo.+ Ngakhale munthu atamufuulira, iye sayankha. Sapulumutsa munthu kumavuto ake.+
7 Manja ali nawo, koma sakhudza kanthu.+Mapazi ali nawo koma sayenda.+Satulutsa mawu ndi mmero wawo.+
46 Beli+ wawerama+ ndipo Nebo wagwada. Mafano awo+ akhala katundu wa nyama zakutchire ndi wa nyama zoweta. Mafanowo angokhala katundu wolemera kwa nyama zotopa.
7 Iwo amamunyamula pamapewa awo.+ Amamutenga n’kukamuika pamalo ake ndi kumuimika bwinobwino. Mulunguyo sayenda kuchoka pamalo akewo.+ Ngakhale munthu atamufuulira, iye sayankha. Sapulumutsa munthu kumavuto ake.+