2 Mafumu 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye anatentha nyumba ya Yehova,+ nyumba ya mfumu,+ nyumba zonse za mu Yerusalemu,+ ndi nyumba ya munthu aliyense wotchuka.+ Yeremiya 52:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye anatentha nyumba ya Yehova,+ nyumba ya mfumu ndi nyumba zonse za mu Yerusalemu.+ Anatenthanso nyumba iliyonse ya munthu wotchuka.+ Hoseya 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Isiraeli anaiwala amene anamupanga+ ndipo anayamba kumanga akachisi.+ Yuda nayenso anachulukitsa mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri.+ Koma ine ndidzatumiza moto m’mizinda yake ndipo udzanyeketsa nsanja zokhalamo za mumzinda uliwonse.”+
9 Iye anatentha nyumba ya Yehova,+ nyumba ya mfumu,+ nyumba zonse za mu Yerusalemu,+ ndi nyumba ya munthu aliyense wotchuka.+
13 Iye anatentha nyumba ya Yehova,+ nyumba ya mfumu ndi nyumba zonse za mu Yerusalemu.+ Anatenthanso nyumba iliyonse ya munthu wotchuka.+
14 Isiraeli anaiwala amene anamupanga+ ndipo anayamba kumanga akachisi.+ Yuda nayenso anachulukitsa mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri.+ Koma ine ndidzatumiza moto m’mizinda yake ndipo udzanyeketsa nsanja zokhalamo za mumzinda uliwonse.”+