Miyambo 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kunyada kumafikitsa munthu ku chiwonongeko,+ ndipo mtima wodzikuza umachititsa munthu kupunthwa.+ Yesaya 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti ilo ndi tsiku la Yehova wa makamu.+ Tsikulo lidzafikira aliyense wodzitukumula ndi wodzikweza. Lidzafikiranso aliyense wokwezeka kapena wotsika.+ Ezekieli 28:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Wachulukitsa chuma chako+ chifukwa chakuti uli ndi nzeru zochuluka+ komanso umachita malonda.+ Chotero mtima wako wayamba kudzikuza chifukwa cha chuma chakocho.”’+
12 Pakuti ilo ndi tsiku la Yehova wa makamu.+ Tsikulo lidzafikira aliyense wodzitukumula ndi wodzikweza. Lidzafikiranso aliyense wokwezeka kapena wotsika.+
5 Wachulukitsa chuma chako+ chifukwa chakuti uli ndi nzeru zochuluka+ komanso umachita malonda.+ Chotero mtima wako wayamba kudzikuza chifukwa cha chuma chakocho.”’+