Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 anapitiriza kuwauza kuti: “Ganizirani mofatsa mawu onse amene ndikulankhula mokuchenjezani lero,+ ndipo muuze ana anu kuti aonetsetse kuti akuchita zimene mawu onse a chilamulo ichi akunena.+

  • 2 Mbiri 11:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Koma anthu a m’mafuko onse a Isiraeli amene anali ndi mtima wofunafuna Yehova Mulungu wa Isiraeli, anatsatira ansembe ku Yerusalemu+ kukapereka nsembe+ kwa Yehova Mulungu wa makolo awo.

  • Miyambo 24:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Choncho ine nditaona zimenezi, ndinayamba kuziganizira mumtima mwanga,+ ndipo ndinaphunzirapo* kuti:+

  • Ezekieli 40:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Tsopano munthuyo anayamba kulankhula nane kuti: “Iwe mwana wa munthu,+ ona ndi maso ako, imva ndi makutu ako, ndipo uike mtima wako pa zonse zimene ndikuonetse, chifukwa wabweretsedwa kuno kuti ine ndikuonetse zinthu zimenezi. Ukauze nyumba ya Isiraeli zonse zimene uone kuno.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena