2 Mafumu 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye anatentha nyumba ya Yehova,+ nyumba ya mfumu,+ nyumba zonse za mu Yerusalemu,+ ndi nyumba ya munthu aliyense wotchuka.+ Salimo 120:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Adzakupatsa mivi yakuthwa ya munthu wamphamvu,+Pamodzi ndi makala amoto a mtengo wa m’chipululu.+ Salimo 140:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Muwakhuthulire makala oyaka moto pamutu pawo.+Muwachititse kugwera m’moto+ ndi m’madzi akuya kuti asanyamukenso.+ Chivumbulutso 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma nthawi yomweyo, mngeloyo anatenga chiwiya chofukiziramo chija, n’kudzazamo moto+ umene anapala paguwa lansembe, ndi kuuponyera kudziko lapansi.+ Ndiyeno kunagunda mabingu,+ kunamveka mawu, ndipo kunachita mphezi+ ndi chivomezi.+
9 Iye anatentha nyumba ya Yehova,+ nyumba ya mfumu,+ nyumba zonse za mu Yerusalemu,+ ndi nyumba ya munthu aliyense wotchuka.+
10 Muwakhuthulire makala oyaka moto pamutu pawo.+Muwachititse kugwera m’moto+ ndi m’madzi akuya kuti asanyamukenso.+
5 Koma nthawi yomweyo, mngeloyo anatenga chiwiya chofukiziramo chija, n’kudzazamo moto+ umene anapala paguwa lansembe, ndi kuuponyera kudziko lapansi.+ Ndiyeno kunagunda mabingu,+ kunamveka mawu, ndipo kunachita mphezi+ ndi chivomezi.+