Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 3:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Chotero ndinanyamuka n’kupita kuchigwako. Kumeneko ndinangoona kuti ulemerero wa Yehova waimirira,+ ngati ulemerero umene ndinauona pafupi ndi mtsinje wa Kebara.+ Nditaona zimenezo, ndinagwada n’kuwerama mpaka nkhope yanga pansi.+

  • Ezekieli 43:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Zimene ndinaonazo zinali zofanana ndi zimene ndinaona m’masomphenya ena.+ Zinali zofanana ndi masomphenya amene ndinaona pamene ndinapita kukawononga mzinda.*+ Ndinaona zinthu zofanana ndi zimene ndinaona m’mphepete mwa mtsinje wa Kebara.+ Nditaona zimenezo, ndinagwada n’kuwerama mpaka nkhope yanga pansi.

  • Danieli 8:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Chotero iye anabwera pafupi ndi pamene ine ndinaima. Atafika, ndinachita mantha ndipo ndinagwada n’kuwerama mpaka nkhope yanga pansi. Ndiyeno anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu,+ dziwa+ kuti masomphenyawa ndi okhudza nthawi ya mapeto.”+

  • Chivumbulutso 1:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Nditamuona, ndinagwa pamapazi ake ngati kuti ndafa.

      Ndipo anandigwira ndi dzanja lake lamanja ndi kundiuza kuti: “Usachite mantha.+ Ine ndine Woyamba+ ndi Wotsiriza,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena