Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 58:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 58 “Fuula mwamphamvu! Usabweze mawu.+ Kweza mawu ako ngati lipenga,+ ndipo uza anthu anga za kupanduka kwawo. A nyumba ya Yakobo uwauze machimo awo.

  • Ezekieli 20:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Kodi ndiwe wokonzeka kuwaweruza? Kodi uwaweruza, iwe mwana wa munthu?+ Auze zinthu zonyansa zimene makolo awo anachita.+

  • Ezekieli 22:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Iwe mwana wa munthu, kodi ndiwe wokonzeka kuweruza?+ Kodi uweruza mzinda umene uli ndi mlandu wa magaziwu+ ndi kuudziwitsa zonyansa zake zonse?+

  • Ezekieli 23:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Yehova anandiuzanso kuti: “Iwe mwana wa munthu, kodi uweruza+ Ohola ndi Oholiba+ ndi kuwauza zinthu zonyansa zimene achita?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena