2 Mbiri 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 inu mumve muli kumwamba+ ndipo muchitepo kanthu+ mwa kusonyeza amene ali wolakwa pom’bwezera temberero lake,+ ndi kusonyeza amene ali wolungama+ pom’patsa mphoto malinga ndi chilungamo chake.+ Ezekieli 33:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Choncho iwe mwana wa munthu, uza nyumba ya Isiraeli kuti, ‘Anthu inu mwanena kuti: “Tingakhale bwanji ndi moyo, popeza kuti kupanduka kwathu ndi machimo athu zili pa ife ndipo tikuwola+ chifukwa cha zimenezi?”’+ Aroma 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Aliyense wochita zoipa, kuyambira Myuda+ mpaka Mgiriki,+ adzaona nsautso ndi zowawa. Agalatiya 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Musanyengedwe,+ Mulungu sapusitsika.+ Chilichonse chimene munthu wafesa, adzakololanso chomwecho.+
23 inu mumve muli kumwamba+ ndipo muchitepo kanthu+ mwa kusonyeza amene ali wolakwa pom’bwezera temberero lake,+ ndi kusonyeza amene ali wolungama+ pom’patsa mphoto malinga ndi chilungamo chake.+
10 “Choncho iwe mwana wa munthu, uza nyumba ya Isiraeli kuti, ‘Anthu inu mwanena kuti: “Tingakhale bwanji ndi moyo, popeza kuti kupanduka kwathu ndi machimo athu zili pa ife ndipo tikuwola+ chifukwa cha zimenezi?”’+