2 Samueli 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho ngakhale mwamuna wolimba mtima amene ali ndi mtima ngati wa mkango+ adzafooka+ ndithu. Izi zili choncho chifukwa Isiraeli yense akudziwa kuti bambo wako ndi mwamuna wamphamvu,+ ngatinso mmene alili amuna olimba mtima amene ali naye.+ Salimo 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ikani mantha m’mitima yawo, inu Yehova,+Kuti anthu a mitundu ina adziwe kuti iwo ndi anthu ochokera kufumbi.+ [Seʹlah.]
10 Choncho ngakhale mwamuna wolimba mtima amene ali ndi mtima ngati wa mkango+ adzafooka+ ndithu. Izi zili choncho chifukwa Isiraeli yense akudziwa kuti bambo wako ndi mwamuna wamphamvu,+ ngatinso mmene alili amuna olimba mtima amene ali naye.+
20 Ikani mantha m’mitima yawo, inu Yehova,+Kuti anthu a mitundu ina adziwe kuti iwo ndi anthu ochokera kufumbi.+ [Seʹlah.]