Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 51:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Babulo wakhala kapu yagolide m’dzanja la Yehova+ ndipo waledzeretsa dziko lonse lapansi.+ Mitundu ya anthu yaledzera ndi vinyo wake.+ N’chifukwa chake mitundu ya anthu ikuchita zinthu zamisala.+

  • Danieli 2:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 inuyo amene Mulungu wakupatsani+ nyama zakutchire ndi mbalame zam’mlengalenga kulikonse kumene kuli anthu, amene Mulungu wakuikani kukhala wolamulira zonsezo, inuyo ndiye mutu wagolide.+

  • Danieli 4:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Mtengowo ndinuyo mfumu,+ chifukwa mwakula ndipo mwakhala ndi mphamvu. Ulemerero wanu wakula mpaka kufika kumwamba+ ndipo ulamuliro wanu wafika kumalekezero a dziko lapansi.+

  • Danieli 7:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Chilombo choyamba chinali chooneka ngati mkango+ ndipo chinali ndi mapiko a chiwombankhanga.+ Ndinapitiriza kuchiyang’ana kufikira pamene mapiko ake anathotholedwa. Ndiyeno anachitukula padziko lapansi+ ndipo anachiimiritsa ndi miyendo iwiri ngati munthu. Kenako chinapatsidwa mtima wa munthu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena