2 Mafumu 17:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Anasiya malamulo onse+ a Yehova Mulungu wawo n’kudzipangira zifaniziro ziwiri za ana a ng’ombe,+ zopangidwa ndi zitsulo zosungunula,+ komanso mzati wopatulika.+ Anayamba kugwadira khamu lonse la zinthu zakuthambo+ ndi kutumikira Baala.+ Hoseya 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Pamene iye anali kuitanidwa kwambiri,+ m’pamenenso anapitiriza kuchoka.+ Anayamba kupereka nsembe kwa zifaniziro za Baala+ ndipo anayamba kufukiza nsembe zautsi kwa zifaniziro zogoba.+
16 Anasiya malamulo onse+ a Yehova Mulungu wawo n’kudzipangira zifaniziro ziwiri za ana a ng’ombe,+ zopangidwa ndi zitsulo zosungunula,+ komanso mzati wopatulika.+ Anayamba kugwadira khamu lonse la zinthu zakuthambo+ ndi kutumikira Baala.+
2 “Pamene iye anali kuitanidwa kwambiri,+ m’pamenenso anapitiriza kuchoka.+ Anayamba kupereka nsembe kwa zifaniziro za Baala+ ndipo anayamba kufukiza nsembe zautsi kwa zifaniziro zogoba.+