Yeremiya 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mikango yamphamvu imamubangulira.+ Imamutulutsira mawu awo.+ Ndipo yapangitsa dziko lake kukhala chinthu chodabwitsa kwa ena. Mizinda yake aiyatsa moto, choncho simukukhala munthu aliyense.+ Yeremiya 50:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Isiraeli ndi nkhosa yosochera.+ Mikango ndi imene yamuchititsa kuthawa.+ Poyamba, mfumu ya Asuri inadya Isiraeli,+ ndipo ulendo uno Nebukadirezara mfumu ya ku Babulo yakukuta mafupa ake.+
15 Mikango yamphamvu imamubangulira.+ Imamutulutsira mawu awo.+ Ndipo yapangitsa dziko lake kukhala chinthu chodabwitsa kwa ena. Mizinda yake aiyatsa moto, choncho simukukhala munthu aliyense.+
17 “Isiraeli ndi nkhosa yosochera.+ Mikango ndi imene yamuchititsa kuthawa.+ Poyamba, mfumu ya Asuri inadya Isiraeli,+ ndipo ulendo uno Nebukadirezara mfumu ya ku Babulo yakukuta mafupa ake.+