Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Tsopano ana aamuna a Eli anali anthu opanda pake.+ Iwo anali kunyalanyaza Yehova.+

  • Ezekieli 22:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Ansembe ako aphwanya chilamulo changa modzionetsera,+ ndipo akuipitsa malo anga oyera.+ Sakusiyanitsa+ zinthu zoyera ndi zinthu wamba.+ Sanauze anthu kusiyana kwa zinthu zodetsedwa ndi zinthu zoyera.+ Anyalanyaza sabata langa+ ndipo andichitira mwano pakati pawo.+

  • Mika 3:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Tamverani izi inu atsogoleri a nyumba ya Yakobo komanso inu olamulira a nyumba ya Isiraeli,+ amene mukuipidwa ndi chilungamo ndiponso amene mukupotoza chilichonse chowongoka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena