Ekisodo 29:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 “Chotero ndidzaonekera pamenepo kwa ana a Isiraeli, ndipo malo amenewa adzayeretsedwa ndi ulemerero wanga.+ Salimo 29:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Liwu la Yehova likuchititsa mbawala zazikazi kuphiriphitha ndi ululu wa pobereka,+Ndipo likufafaniza nkhalango.+M’kachisi wake aliyense akunena kuti: “Ulemerero ndi wa Mulungu!”+ Yesaya 60:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Ulemerero wa Lebanoni udzabwera kwa iwe. Mtengo wofanana ndi mkungudza, mtengo wa ashi, ndiponso mtengo wa paini zidzabwera pa nthawi imodzi,+ kuti zikongoletse malo anga opatulika,+ ndipo ine ndidzalemekeza malo oikapo mapazi anga.+
43 “Chotero ndidzaonekera pamenepo kwa ana a Isiraeli, ndipo malo amenewa adzayeretsedwa ndi ulemerero wanga.+
9 Liwu la Yehova likuchititsa mbawala zazikazi kuphiriphitha ndi ululu wa pobereka,+Ndipo likufafaniza nkhalango.+M’kachisi wake aliyense akunena kuti: “Ulemerero ndi wa Mulungu!”+
13 “Ulemerero wa Lebanoni udzabwera kwa iwe. Mtengo wofanana ndi mkungudza, mtengo wa ashi, ndiponso mtengo wa paini zidzabwera pa nthawi imodzi,+ kuti zikongoletse malo anga opatulika,+ ndipo ine ndidzalemekeza malo oikapo mapazi anga.+