Levitiko 26:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndidzathyola kunyada kwanuko, ndi kuchititsa kumwamba kukhala ngati chitsulo+ ndi nthaka yanu ngati mkuwa. Deuteronomo 28:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Thambo limene lili pamwamba pa mutu wako lidzakhala ngati mkuwa, ndipo nthaka yako idzakhala ngati chitsulo.+ 1 Mafumu 8:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 “Kumwamba kukatsekeka, mvula n’kumakanika kugwa+ chifukwa choti anali kukuchimwirani,+ ndiyeno iwo n’kupemphera atayang’ana malo ano,+ ndi kutamanda dzina lanu ndiponso kusiya tchimo lawo chifukwa choti mwakhala mukuwasautsa,+
19 Ndidzathyola kunyada kwanuko, ndi kuchititsa kumwamba kukhala ngati chitsulo+ ndi nthaka yanu ngati mkuwa.
23 Thambo limene lili pamwamba pa mutu wako lidzakhala ngati mkuwa, ndipo nthaka yako idzakhala ngati chitsulo.+
35 “Kumwamba kukatsekeka, mvula n’kumakanika kugwa+ chifukwa choti anali kukuchimwirani,+ ndiyeno iwo n’kupemphera atayang’ana malo ano,+ ndi kutamanda dzina lanu ndiponso kusiya tchimo lawo chifukwa choti mwakhala mukuwasautsa,+