Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Hagai 1:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 1 M’chaka chachiwiri cha ulamuliro wa Mfumu Dariyo,+ m’mwezi wa 6, pa tsiku loyamba la mweziwo, mawu a Yehova anafika kwa Zerubabele+ mwana wa Salatiyeli+ bwanamkubwa wa Yuda,+ ndi kwa Yoswa+ mwana wa Yehozadaki+ mkulu wa ansembe. Mawuwa anafika kwa anthu amenewa kudzera mwa mneneri Hagai+ kuti:

  • Hagai 2:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “‘Koma tsopano limba mtima iwe Zerubabele. Limba mtima+ iwe Yoswa mwana wa Yehozadaki mkulu wa ansembe,’ watero Yehova.

      “‘Limbani mtima anthu nonse a m’dzikoli ndipo gwirani ntchito,’+ watero Yehova.

      “‘Pakuti ine ndili ndi inu,’+ watero Yehova wa makamu.

  • Zekariya 3:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pamenepo ndinanena kuti: “Auzeni kuti amuveke nduwira* yoyera kumutu kwake.”+ Ndipo anamuvekadi nduwira yoyera kumutu kwake. Anamuvekanso zovala. Apa n’kuti mngelo wa Yehova ataimirira pambali pake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena