Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Maliko 15:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Ndiyeno Yosefe anagula nsalu yabwino kwambiri ndi kumutsitsa. Atatero anamukulunga ndi nsalu yabwino kwambiri ija ndi kumuika+ m’manda+ amene anawasema m’thanthwe. Anagubuduza chimwala ndi kutseka pakhomo la manda achikumbutsowo.+

  • Luka 23:53
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 53 Choncho anautsitsa+ ndi kuukulunga munsalu yabwino kwambiri, kenako anakauika m’manda+ ogobedwa muthanthwe, mmene anali asanaikemo munthu chikhalire.+

  • Yohane 19:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Choncho iwo anatenga mtembo wa Yesu n’kuukulunga ndi nsalu zamaliro zonunkhira,+ malinga ndi mwambo umene Ayuda anali kutsatira poika maliro.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena