Luka 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Uli ngati chofufumitsa chimene mayi wina anachitenga ndi kuchibisa mu ufa wokwana mbale zoyezera zazikulu zitatu, moti mtanda wonsewo unafufuma.”+ 1 Akorinto 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chimene mukudzitamira+ si chabwino ayi. Kodi simukudziwa kuti chofufumitsa chaching’ono chimafufumitsa+ mtanda wonse?+ Agalatiya 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chofufumitsa chaching’ono chimafufumitsa mtanda wonse.+
21 Uli ngati chofufumitsa chimene mayi wina anachitenga ndi kuchibisa mu ufa wokwana mbale zoyezera zazikulu zitatu, moti mtanda wonsewo unafufuma.”+
6 Chimene mukudzitamira+ si chabwino ayi. Kodi simukudziwa kuti chofufumitsa chaching’ono chimafufumitsa+ mtanda wonse?+