Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 33:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Iye analinso kukonda anthu ake.+

      Oyera awo onse ali m’manja mwanu.+

      Iwowa anakhala pansi, pamapazi panu.+

      Anayamba kulandira ena mwa mawu anu.+

  • Luka 8:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Zitatero anthu anabwera kudzaona zomwe zachitikazo. Atafika kwa Yesu anapeza munthu amene anam’tulutsa ziwanda uja atakhala pansi pafupi ndi Yesu. Anamupeza atavala bwino komanso maganizo ake ali bwinobwino, ndipo iwo anachita mantha.+

  • Machitidwe 22:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Inetu ndine Myuda,+ wobadwira ku Tariso wa ku Kilikiya,+ koma ndinaphunzitsidwa ndi Gamaliyeli+ mumzinda womwe uno. Anandiphunzitsa kutsatira Chilamulo cha makolo athu mokhwimitsa zinthu kwambiri.+ Ndipo ndinali wodzipereka+ potumikira Mulungu monga mmene nonsenu mulili lero.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena