26 Pa maulendo kawirikawiri, zoopsa za m’mitsinje, zoopsa za achifwamba pamsewu,+ zoopsa zochokera kwa anthu a mtundu wanga,+ zoopsa zochokera kwa anthu a mitundu ina,+ zoopsa mumzinda,+ zoopsa m’chipululu, zoopsa za panyanja, zoopsa pakati pa abale onyenga,