Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 6:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Zitatero mfumuyo inalamula kuti abweretse Danieli. Atabwera naye anamuponya m’dzenje la mikango.+ Koma mfumu inauza Danieli kuti: “Mulungu wako amene umamutumikira mosalekeza akupulumutsa.”+

  • Machitidwe 5:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Koma usiku, mngelo wa Yehova+ anatsegula zitseko za ndendeyo+ ndi kuwatulutsa, ndipo anawauza kuti:

  • Machitidwe 23:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Koma tsiku lomwelo usiku, Ambuye anaimirira pambali pake+ ndi kunena kuti: “Limba mtima!+ Pakuti wandichitira umboni mokwanira+ mu Yerusalemu, ndipo ukandichitiranso umboni ku Roma.”+

  • Aheberi 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kodi angelo onse si mizimu+ yotumikira ena,+ yotumidwa kukatumikira amene adzalandire chipulumutso monga cholowa chawo?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena