Machitidwe 13:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Koma Ayuda+ anauza zoipa amayi otchuka amene anali opembedza Mulungu, komanso amuna olemekezeka a mumzindawo. Chotero iwowa anachititsa kuti Paulo ndi Baranaba ayambe kuzunzidwa,+ ndipo anawaponya kunja kwa mzinda wawo. 1 Akorinto 15:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kodi ifeyo tikuikiranji moyo wathu pachiswe nthawi zonse?+ 2 Akorinto 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndi atumiki a Khristu kapena? Ndikuyankha ngati wamisala, ineyo ndiye weniweni woposanso iwowo:+ m’ntchito zovuta mowirikiza koposa,+ m’ndende osachita kunena,+ kumenyedwa kosawerengeka, kutsala pang’ono kufa kawirikawiri.+ Afilipi 2:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chotero, mulandireni monga mwa nthawi zonse,+ mwa Ambuye ndi chimwemwe chonse. Ndipo abale okhala ngati iyeyu muziwalemekeza kwambiri,+
50 Koma Ayuda+ anauza zoipa amayi otchuka amene anali opembedza Mulungu, komanso amuna olemekezeka a mumzindawo. Chotero iwowa anachititsa kuti Paulo ndi Baranaba ayambe kuzunzidwa,+ ndipo anawaponya kunja kwa mzinda wawo.
23 Ndi atumiki a Khristu kapena? Ndikuyankha ngati wamisala, ineyo ndiye weniweni woposanso iwowo:+ m’ntchito zovuta mowirikiza koposa,+ m’ndende osachita kunena,+ kumenyedwa kosawerengeka, kutsala pang’ono kufa kawirikawiri.+
29 Chotero, mulandireni monga mwa nthawi zonse,+ mwa Ambuye ndi chimwemwe chonse. Ndipo abale okhala ngati iyeyu muziwalemekeza kwambiri,+