Deuteronomo 32:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+Njira zake zonse ndi zolungama.+Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita chosalungama.+Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+ 2 Mbiri 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno anauza oweruzawo kuti: “Samalani zochita zanu+ chifukwa simukuweruzira munthu koma mukuweruzira Yehova,+ ndipo iye ali nanu pa ntchito yoweruzayi.+ Yobu 34:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho inu amuna a mtima+ womvetsa zinthu, ndimvereni.Mulungu woona sangachite zoipa m’pang’ono pomwe,+Ndipo Wamphamvuyonse sangachite zinthu zopanda chilungamo ngakhale pang’ono.+
4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+Njira zake zonse ndi zolungama.+Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita chosalungama.+Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+
6 Ndiyeno anauza oweruzawo kuti: “Samalani zochita zanu+ chifukwa simukuweruzira munthu koma mukuweruzira Yehova,+ ndipo iye ali nanu pa ntchito yoweruzayi.+
10 Choncho inu amuna a mtima+ womvetsa zinthu, ndimvereni.Mulungu woona sangachite zoipa m’pang’ono pomwe,+Ndipo Wamphamvuyonse sangachite zinthu zopanda chilungamo ngakhale pang’ono.+