Machitidwe 17:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho anamugwira n’kupita naye kubwalo la Areopagi, ndi kunena kuti: “Kodi tingadziweko za chiphunzitso chatsopanochi+ chimene iwe ukuphunzitsa? 1 Akorinto 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma munthu wokonda zinthu za m’dziko* salandira zinthu za mzimu wa Mulungu, chifukwa amaziona ngati zopusa ndipo sangathe kuzidziwa,+ chifukwa zimafuna kuzifufuza mwauzimu. 1 Akorinto 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu asamadzinyenge yekha: Ngati aliyense wa inu akudziyesa wanzeru+ mu nthawi* ino, akhale wopusa kuti akhale wanzeru.+
19 Choncho anamugwira n’kupita naye kubwalo la Areopagi, ndi kunena kuti: “Kodi tingadziweko za chiphunzitso chatsopanochi+ chimene iwe ukuphunzitsa?
14 Koma munthu wokonda zinthu za m’dziko* salandira zinthu za mzimu wa Mulungu, chifukwa amaziona ngati zopusa ndipo sangathe kuzidziwa,+ chifukwa zimafuna kuzifufuza mwauzimu.
18 Munthu asamadzinyenge yekha: Ngati aliyense wa inu akudziyesa wanzeru+ mu nthawi* ino, akhale wopusa kuti akhale wanzeru.+